African Evangelical Church and Ndirande Police station have vowed to work together in order to intensify the fight against gender-based violence in the area. The Victim Support Unit desk under the Community policing branch took the campaign to the church which is located in the area of Group village headman Somanje Makata with an aim of sensitizing the female congregates ...
Read More »Author Archives: john
WE FOLLOWED ALL TENDER PROCEDURES, WE ARE APOLITICAL-Mia brother speaks on Dodma goat contract
AWS Trucking, a company belonging to the late Sidik Mia’s brother, which has won MK836 million tender to supply goats to the Department of Disaster Management Affair (DoDMA), says the company is apolitical. The Company’s managing director, Mr. Khalid Mia told Malawi Voice on Thursday amidst rumors on the social media indicating that DoDMA awarded the multi-million kwacha tender to ...
Read More »Chakwera Anaphwanya Malamulo-Court
Bwalo la High Court lati President Lazarus Chakwera anaphwanya malamulo pobwezeletsa pa mpando Noah Dalasi ngati mfumu yaikulu Ngabu ya m’boma la Chikwawa. Oweruza mlandu Justice Mandala Mambulatsa ndi yemwe wapereka chigamulochi la Chiwiri ponena kuti kubwezeletsedwa kwa a Dalasi kunali kotsatsata malamulo a dziko lino. Justice Mandala Mambulatsa walamulanso President Lazarus Chakwera apereke ndalama zonse zomwe zagwiritsidwa ndi mbali ...
Read More »‘Alipire Chindapusa Kaamba ka Chamba’
Bwalo la Milandu la Lisungwi m’boma la Neno lalamula anyamata atatu kupereka chindaputsa cha ndalama zokwana K200,000 aliyense atapezeka olakwa pa mlandu opezeka ndi fodya wa mkulu wa Chamba opanda kalata za chiloledzo. Atatuwa ndi a John White, William Ndalama komanso Stonald Kazembe a zaka zapakati pa 20 ndi 22, ndipo anamangidwa pa malo opangira chipikitcheni cha apolisi cha Zalewa aliyense ...
Read More »Malawi Govt to Promote Use of Clean Energy Sources Among People
There are high expectations that efforts to have ‘clean energy’ in the country will fully take their shape as authorities are working tirelessly to have the dreams achieved. Among other interventions, the authorities are creating a friendly environment for the production of the energy type that has for a long time been coming under criticism for lack of proper direction. ...
Read More »Robert Mugabe Aikidwanso M’manda
Bwalo la milandu m’dziko la Zimbabwe lagwirizana ndi chigamulo cha mfumu Zvimba ya kumeneko choti thupi la mtsogoleri wakale wa dzikoli, Robert Mugabe alifukule ndipo liikidwenso m’maso. Mfumu Zvimba inati thupili silinaikidwe m’manda mwa Ulemu wake komanso linaikidwa ku manda a banja koma mwa ndondomeko yake, limayenera kukaikidwa ku manda omwe anthu olemekezeka amaikidwa. Komatu ana a malemu Robert Mugabe ...
Read More »Amenyedwa ndi Mpini Kaamba ka M’memo
Mnyamata wina ku Chilomoni ali ku chipatala komwe akulandira thandizo la mankhwala, mnzake wina atamumenya ndi mpini ati kaamba koti amafuna kudya nawo nsima ya m’memo omwe sanasonkhe. Yemwe watitumizira nkhani-yi wati monga mwa nthawi zonse amnayamatawa asonkha ndalama ya m’memo wa tsikuli koma m’modzi mwa iwo sanasonkhe ngakhale pa nthawi ya kudya anali liki-liki kufuna kudya nawo zomwe zinakwiyitsa ...
Read More »A Mpinganjira ndi a Ziphuphu
Mpondamatiki Thom Mpinganjira wapezeka olakwa pa milandu iwiri mwa milandu isanu ndi Umodzi yokhuza kuchita upo ofuna kupereka ziphuphu kwa oweruza asanu omwe amanva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha mu 2019. Bungwe la ACB linatengera ku bwalolo a Mpinganjira, oweluzawa atakamang’ala ku bungweli ponena kuti mkuluyu amafuna kuwakopa kuti akondere mbali ya odandaulidwa pa mlanduwo omwe anali mtsogoleri wakale ...
Read More »Gule Wamkulu Under Fire In Dedza
Dedza, September 7, Malawi News Agency Story: Gule wamkulu from Traditional Authority Chilikumwendo in Dedza has been accused of disrupting Safe-spaces sessions which are conducted for adolescent girls and young women. The accusation emerged on Monday during a review meeting conducted at Katewe Teachers Development Centre (TDC) for focal persons and mentors who conduct the sessions under the ‘Action for Adolescent Girls and Young ...
Read More »Police Shot Dead a Suspected Robber in Mzuzu
A suspected robber has last night been shot dead by police when he was attempting to steal in one of the shops at Luwinga Industrial Area. A spokesperson for the Mzuzu police, Paul Tembo has confirmed the shooting clarifying that it was in defense of the men in uniform as the robber charged them with a panga knife. He has ...
Read More »