DonZo – FiluuMaster – Chikwangwani

Download “DonZo - FiluuMaster - Chikwangwani” – Downloaded 0 times –

 

*_DonZo – CHIKWANGWANI Lyrics_*

_who Do *You* think *I Am*?_

So the other day, I think it was a Saturday/
N’nali ndiku bhang’a, kuvaya pa dheni, ndili chamu High Way_ n’nangomva mwa bwaiy awiri kukambilana_
Here’s a little bit of what I heard em say/
Akuti “Man!! Ndiyemweyo – musandiseke,
Chabwino let’s ask his name …Funsa/
Anali akutsutsana_
If maybe I just looked the same as ” *who*? kaya/
The other one was certain, and that there was no mistaking_
The other was a skeptic_
Ine n’nali ndikungodutsa ka/
The other was explaining akuti ‘kodi _iweyo_ sun’tsata?_
Kodi _iweyo_ sungathaimile olo move,
Olo kum’dziwila utamungomuonela kunsana?/
The other was like ‘mmh mayazi,! mesa amapezekela ku LLz mfanayi?, _iweyo_ how can you tell kuti ndiyemwe uja amaspita za Faya zi πŸ”₯? Sukundisuntha apa_/
Wina uja akuti “aah man, munthu sasamuka?
Chabwino sasanduka, koma sankakuwuzani? kuti _iyeyo_ anazipatula_
Amati akangoyasamula- Beat kuphwasamula_/
Siosowa munthu uja, tampatsa (shapu, bhoo, shuwa?)/
And then these 2 niqqaz approached *Me* – Nazandikodola…/
Nde anayamba nkundipatsa moni, nkuzati pali ka funso koti ‘Kodi ndioyimba uti ndimati ndikakhala Amandidolola?/
Not only that, koma ‘kodi ndinayamba ndaziona?’_
Nkuzifananiza ndi artist wanji – Oblowa kaya NgObhowa ../
Amafuna ntazilongosola – adziwe zoona, kenako adzipita atatsimikiza!!/
Kwenikweni chomwe anandidziwila sindikuchidziwa_
Nangozindikila akuti ” Eti man, Kodi inuyo, siinu a *DonZo*?/
A *DonZo* timangowawona m’ma Photos,_
Osati kwenikweni Kuma Shows coz_
Sapanga appear kuti Ali active on all those_
Social media platforms_/
Olo m’ma Videos_
We never see him at the club_
He’s off the map_
Kodi Ali mu M-Dubz?/
Timangomva mphekesela kuti _Anapenga_ πŸ€” panopa anapepela 🀣/
Ngati Ali Dolo bwanji samamvekela pa radio olo pa kanema?_ Nde tangonena, Anyamula bwanji mbendela?
Kodi _iyeyo_ nzakuti.. amatchena?/
Azimzake akale kale achina *Chariz* sacheza naye?
Zinakhala bwanji kuti amuyiwale?
Pamenepopo inuyo mutiyankhe!!_
Mukantelo – nkhaniyi mwina ingathe../
Inu Ndikumathelo – Ngati Kartel – UTeacha munayamba pakale_/
Takutayilani ka Mtengo – Mumatha inu – Ma Rappers akunama nawe Wena!!!/
Bwanji sukufuna ukambe? Nena..!/
Kwenikweni bwanji simpeZeka pakati pama famous artists?, Simutha kucheza?/
Pama charts olo kukhalako *#1*, mulibe plan Kodi?_ ndekuti simuzitengela?/
Tinamva kuti munagela mpaka gala, tsono bwanji simuzinenelela?/
Kusamenya ma collabo ndiomba ena Ku, kumakhala kuti mukuwaphweketsa?/
Kuopa kuwatchukitsa kuti ajoina ka gulu Kama artist owaphulitsa- paja anawa amangodyedwa?/
Kodi bwanji mudakali otsalila?_
Bwanji mukuchedwa?/
Kodi man, ndinuyodi ? Kapena tidikile ena…?
Tamayankhani ka, nyimboyi yatha kale iyi..

Eeh chikwangwani…
Ndine Chikwangwani…

I point you in the right direction.. I think ..

Apa nde udziwa kale
after ma bwaiy aja atandifunsa funsa.. ineyo n’nangowayang’ana nkungoti “aah Ndiineyo 😌 ”

Kenako basi kwinako tizacheza mu *Chikwangwani pt 2*

Please follow and like us:
Pin Share
(Visited 248 times, 1 visits today)

RSS
Follow by Email