Mista Kozmik – Mwai Mwamwa Simbota(Prod Chawabeats)

Download “Mista Kozmik - Mwai Mwamwa Simbota(Prod Chawabeats)”

1.Mista-Kozmik-Mwamwa-Mwai-SimbotaLoveEmojisEp-1.mp3 – Downloaded 4579 times – 7.30 MB
Mista Kozmik – Mwai Simbota (Mwamwa) Lyrics
Producer : CHAWABEATS
Off “Love & Emojis EP”

HOOK
Nane ndimafuna nkazi ooneka bo //
Azizandifilisaa ngati ndiku show //
Osamongosuta ngati nigga joe//
Osachitisa manyazi pa video call//
I just wanna girl like mwamwa,x2//
Azikagwila ntchito ngati mwamwa/
Slim girl ,wa mawu abo ngati mwamwa //

Verse 1
Sindikufuna nkazi, olowelera//
Oti kupanga naye date pompo kusochera//
Sindikufuna nkazi,omangovuta//
Otii kuyenda naye kugulu nkumakasuta///
Sindikufuna oti azindipasa thensi//
Ngati pa mic kukanika kuyika verse//
Ine ayi, nkazi omangolira //
Obwera kwaine,kuzandithesera calear//

Nkazi waine azizagwila ntchito //
Ananga azavutike iyeyo alipo//
Azakhale business woman, Kaya journalist//
Kaya teacher Kaya azakhala wapolice//

BRIDGE
Ndikufuna wa indipendent, oyima payeka//
Osadalira ine zinthu nkupanga payekha//0
Ndikufuna okhala Paden osati shabini//
Wokongola , wakhalidwe,osangowalira Min//

VERSE 2
Anzanu,ozisata amaphusha Kaye geli//
Sapanga phuma nkumapangano za usleyi//
Amalimbikira Kuti azakhale paboo//
Ndimamuma Dola azizapanga collabo//

Lero Ndikuuzen,
Asamakunamizeni//
Zoti muzagwidwa ndimwamuna wazidola//
Ndati Ndikuuzen, asamakupusiseni//
Inu nkusiya geli busy ndikumakabola//

Mamuna amavuta Ngati ulibe Zi kheeshi//
Atha kukutuluka ndikukuyika pa benchi//
Osaphunzira amazasowa ntendele//
Amakuvutisaa heavy Ngati ulikundende//

BRIDGE
Ndikufuna wa indipendent, oyima payeka//
Osadalira ine zinthu nkupanga payekha//0
Ndikufuna okhala Paden osati shabini//
Wokongola , wakhalidwe,osangowalira Min//

(Visited 142 times, 1 visits today)
Please follow and like us:
Pin Share
RSS
Follow by Email