Mpondamatiki Thom Mpinganjira wapezeka olakwa pa milandu iwiri mwa milandu isanu ndi Umodzi yokhuza kuchita upo ofuna kupereka ziphuphu kwa oweruza asanu omwe amanva mlandu wa chisankho cha mtsogoleri cha mu 2019. Bungwe la ACB linatengera ku bwalolo a Mpinganjira, oweluzawa atakamangโala ku bungweli ponena kuti mkuluyu amafuna kuwakopa kuti akondere mbali ya odandaulidwa pa mlanduwo omwe anali mtsogoleri wakale ...
Read More »